Machitidwe 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:4 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, ptsa. 18-191/15/1990, tsa. 6
4 Pamenepo Koneliyo anayang’anitsitsa mngelo uja, ndipo mantha atamugwira anati: “N’chiyani Mbuyanga?” Mngeloyo anamuuza kuti: “Mapemphero ako+ ndi mphatso zako zachifundo zakwera kwa Mulungu monga chikumbutso.+