Machitidwe 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mngelo amene anali kulankhula nayeyo atangochoka, iye anaitana antchito ake a panyumbapo awiri ndi msilikali. Msilikaliyo anali wopembedza, ndipo anali mmodzi wa amene anali kumutumikira nthawi zonse.+
7 Mngelo amene anali kulankhula nayeyo atangochoka, iye anaitana antchito ake a panyumbapo awiri ndi msilikali. Msilikaliyo anali wopembedza, ndipo anali mmodzi wa amene anali kumutumikira nthawi zonse.+