Machitidwe 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,5/15/1990, tsa. 25
9 Tsiku lotsatira, ulendo wawo uli mkati komanso akuyandikira mzindawo, Petulo anakwera padenga*+ kukapemphera cha m’ma 12 koloko masana.*+