Machitidwe 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 M’masomphenyawo anaona kumwamba kutatseguka,+ ndipo chinthu china chake chinali kutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi n’kumachitsitsira padziko lapansi.
11 M’masomphenyawo anaona kumwamba kutatseguka,+ ndipo chinthu china chake chinali kutsika. Chinthucho chinali chooneka ngati chinsalu chachikulu chimene achigwira m’makona onse anayi n’kumachitsitsira padziko lapansi.