Machitidwe 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma Petulo anati: “Iyayi Ambuye, sindinadyepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chikhalire.”+
14 Koma Petulo anati: “Iyayi Ambuye, sindinadyepo choipitsidwa ndi chonyansa chilichonse chikhalire.”+