Machitidwe 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu amenewo anamvekanso kachitatu, ndipo nthawi yomweyo chinthu chooneka ngati chinsalu chija chinatengedwa kupita kumwamba.+
16 Mawu amenewo anamvekanso kachitatu, ndipo nthawi yomweyo chinthu chooneka ngati chinsalu chija chinatengedwa kupita kumwamba.+