Machitidwe 10:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero ndinawatumiza mwamsanga kwa inu, ndipo mwachita bwino kubwera kuno. N’chifukwa chake pa nthawi ino tonse tili pano pamaso pa Mulungu, kuti timve zonse zimene Yehova wakulamulani kuti mutiuze.”+
33 Chotero ndinawatumiza mwamsanga kwa inu, ndipo mwachita bwino kubwera kuno. N’chifukwa chake pa nthawi ino tonse tili pano pamaso pa Mulungu, kuti timve zonse zimene Yehova wakulamulani kuti mutiuze.”+