Machitidwe 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:4 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 123 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 54
4 Popitiriza ulendo wawo m’mizinda, anali kupatsa okhulupirira a kumeneko malamulo oyenera kuwatsatira, malinga ndi zimene atumwi ndi akulu ku Yerusalemu anagamula.+