Machitidwe 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atangoona masomphenya amenewo, tinaganiza zopita ku Makedoniya.+ Tinali otsimikiza kuti Mulungu watiitana kuti tikalengeze uthenga wabwino kwa anthu akumeneko. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:10 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 12, 126 Nsanja ya Olonda,11/15/2007, ptsa. 18-19
10 Atangoona masomphenya amenewo, tinaganiza zopita ku Makedoniya.+ Tinali otsimikiza kuti Mulungu watiitana kuti tikalengeze uthenga wabwino kwa anthu akumeneko.