Machitidwe 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atafika nawo kwa akuluakulu a boma, ananena kuti: “Anthu awa akusokoneza kwambiri+ mzinda wathu, chikhalirecho iwowa ndi Ayuda. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2150 Nsanja ya Olonda,9/15/1996, tsa. 28
20 Atafika nawo kwa akuluakulu a boma, ananena kuti: “Anthu awa akusokoneza kwambiri+ mzinda wathu, chikhalirecho iwowa ndi Ayuda.