Machitidwe 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa tsiku loyamba+ la mlungu, titasonkhana pamodzi kuti tidye chakudya, Paulo anayamba kuwakambira nkhani, chifukwa anali kunyamuka m’mawa wake. Ndipo anatenga nthawi yaitali akulankhula mpaka pakati pa usiku. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:7 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,2/15/1993, tsa. 294/15/1991, ptsa. 26-27
7 Pa tsiku loyamba+ la mlungu, titasonkhana pamodzi kuti tidye chakudya, Paulo anayamba kuwakambira nkhani, chifukwa anali kunyamuka m’mawa wake. Ndipo anatenga nthawi yaitali akulankhula mpaka pakati pa usiku.