-
Machitidwe 20:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Paulo ali mkati mokamba nkhani, mnyamata wina dzina lake Utiko amene anakhala pawindo, anagona tulo tofa nato. Ali m’tulo choncho, anagwa pansi kuchokera panyumba yachitatu yosanja, ndipo anamupeza atafa.
-