Machitidwe 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Paulo anaganiza zongolambalala Efeso,+ kuti asataye nthawi m’chigawo cha Asia. Anachita zimenezi chifukwa anali kufulumira kuti ngati n’kotheka, akakhale ali ku Yerusalemu+ pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite.
16 Paulo anaganiza zongolambalala Efeso,+ kuti asataye nthawi m’chigawo cha Asia. Anachita zimenezi chifukwa anali kufulumira kuti ngati n’kotheka, akakhale ali ku Yerusalemu+ pa tsiku la chikondwerero cha Pentekosite.