Machitidwe 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 173 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 22
22 Ndipo tsopano, popeza kuti mzimu wandikakamiza,+ ndikupita ku Yerusalemu, ngakhale kuti sindikudziwa zimene zikandichitikire kumeneko.