Machitidwe 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Choncho khalani maso, ndipo kumbukirani kuti kwa zaka zitatu,+ usana ndi usiku, sindinaleke kuchenjeza+ aliyense wa inu ndi misozi. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:31 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 33
31 “Choncho khalani maso, ndipo kumbukirani kuti kwa zaka zitatu,+ usana ndi usiku, sindinaleke kuchenjeza+ aliyense wa inu ndi misozi.