Machitidwe 20:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo anamva chisoni kwambiri, makamaka chifukwa cha mawu amene iye ananena akuti sadzaonanso nkhope yake.+ Kenako anamuperekeza+ kukakwera ngalawa.
38 Iwo anamva chisoni kwambiri, makamaka chifukwa cha mawu amene iye ananena akuti sadzaonanso nkhope yake.+ Kenako anamuperekeza+ kukakwera ngalawa.