Machitidwe 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero munali chisokonezo mumzinda wonsewo, ndipo anthu anali balalabalala+ kuthamangira kukachisiko. Kenako anagwira Paulo ndi kumukokera kunja kwa kachisi.+ Nthawi yomweyo zitseko zinatsekedwa. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:30 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2020, tsa. 31
30 Chotero munali chisokonezo mumzinda wonsewo, ndipo anthu anali balalabalala+ kuthamangira kukachisiko. Kenako anagwira Paulo ndi kumukokera kunja kwa kachisi.+ Nthawi yomweyo zitseko zinatsekedwa.