Machitidwe 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mwamsanga, iye anatenga asilikali ndi akapitawo awo ndi kuthamangira kumeneko.+ Anthuwo ataona mkulu wa asilikali+ uja pamodzi ndi asilikali akewo, analeka kumenya Paulo.
32 Mwamsanga, iye anatenga asilikali ndi akapitawo awo ndi kuthamangira kumeneko.+ Anthuwo ataona mkulu wa asilikali+ uja pamodzi ndi asilikali akewo, analeka kumenya Paulo.