Machitidwe 21:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma ena m’khamulo anayamba kufuula zinthu zina, enanso zina.+ Choncho, atalephera kutolapo mfundo yeniyeni chifukwa cha phokoso, analamula kuti apite naye kumpanda wa asilikali.+
34 Koma ena m’khamulo anayamba kufuula zinthu zina, enanso zina.+ Choncho, atalephera kutolapo mfundo yeniyeni chifukwa cha phokoso, analamula kuti apite naye kumpanda wa asilikali.+