Aroma 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Amunanso chimodzimodzi. Iwo anasiya njira yachibadwa yofuna akazi+ n’kumatenthetsana okhaokha mwachiwawa m’chilakolako choipa, amuna ndi amuna anzawo,+ kuchitirana zonyansa+ ndi kulandiriratu mphoto+ yoyenerera kulakwa kwawo.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:27 Galamukani!,1/2012, tsa. 283/8/1995, tsa. 227/8/1989, ptsa. 30-31 Nsanja ya Olonda,7/15/1997, ptsa. 9-10 Mtendere Weniweni, ptsa. 146-147
27 Amunanso chimodzimodzi. Iwo anasiya njira yachibadwa yofuna akazi+ n’kumatenthetsana okhaokha mwachiwawa m’chilakolako choipa, amuna ndi amuna anzawo,+ kuchitirana zonyansa+ ndi kulandiriratu mphoto+ yoyenerera kulakwa kwawo.+
1:27 Galamukani!,1/2012, tsa. 283/8/1995, tsa. 227/8/1989, ptsa. 30-31 Nsanja ya Olonda,7/15/1997, ptsa. 9-10 Mtendere Weniweni, ptsa. 146-147