Aroma 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiponso, ngati tinafadi limodzi ndi Khristu, timakhulupirira kuti tidzakhalanso ndi moyo limodzi ndi iye.+
8 Ndiponso, ngati tinafadi limodzi ndi Khristu, timakhulupirira kuti tidzakhalanso ndi moyo limodzi ndi iye.+