Aroma 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, ngati zimene sindifuna kuchita ndi zimene ndimachita,+ ndikuvomereza kuti Chilamulo ndi chabwino.+
16 Komabe, ngati zimene sindifuna kuchita ndi zimene ndimachita,+ ndikuvomereza kuti Chilamulo ndi chabwino.+