Aroma 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho abale, tili ndi ngongole, osati kwa thupi kuti tizikhala motsatira zofuna za thupi.+