Aroma 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+ Aroma Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:12 Nsanja ya Olonda,10/1/1989, ptsa. 30-31
12 Usiku uli pafupi kutha, usana wayandikira.+ Chotero tiyeni tivule ntchito za mdima+ ndipo tivale zida za kuwala.+