Aroma 15:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komabe, ndakulemberani mfundo zina mosapita m’mbali kuti ndikukumbutseninso.+ Ndachita zimenezi chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu wandipatsa.+
15 Komabe, ndakulemberani mfundo zina mosapita m’mbali kuti ndikukumbutseninso.+ Ndachita zimenezi chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu wandipatsa.+