1 Akorinto 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi anthu inu mwakhuta kale eti? Mwalemera kale, si choncho?+ Kodi mwayamba kale kulamulira monga mafumu+ popanda ife? Ndikanakondadi mukanayamba kulamulira monga mafumu, kuti ifenso tilamulire limodzi nanu monga mafumu.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2008, tsa. 221/15/1994, ptsa. 17-18
8 Kodi anthu inu mwakhuta kale eti? Mwalemera kale, si choncho?+ Kodi mwayamba kale kulamulira monga mafumu+ popanda ife? Ndikanakondadi mukanayamba kulamulira monga mafumu, kuti ifenso tilamulire limodzi nanu monga mafumu.+