1 Akorinto 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:14 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, tsa. 27
14 Momwemonso, Ambuye anakonza+ kuti olengeza uthenga wabwino azipeza zodzisamalira pa moyo kudzera mwa uthenga wabwino.+