1 Akorinto 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho ndikufuna mudziwe kuti palibe wolankhula mwa mzimu wa Mulungu amene anganene kuti: “Yesu ndi wotembereredwa!”+ Palibenso amene anganene popanda mzimu woyera kuti: “Yesu ndiye Ambuye!”+ 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:3 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, tsa. 21
3 Choncho ndikufuna mudziwe kuti palibe wolankhula mwa mzimu wa Mulungu amene anganene kuti: “Yesu ndi wotembereredwa!”+ Palibenso amene anganene popanda mzimu woyera kuti: “Yesu ndiye Ambuye!”+