1 Akorinto 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’Chilamulo muli mawu akuti: “‘Anthu awa+ ndidzawalankhula m’malilime a alendo,+ ndipo ndidzawalankhula ndi milomo ya anthu achilendo, koma iwo sadzandimverabe,’ watero Yehova.”+
21 M’Chilamulo muli mawu akuti: “‘Anthu awa+ ndidzawalankhula m’malilime a alendo,+ ndipo ndidzawalankhula ndi milomo ya anthu achilendo, koma iwo sadzandimverabe,’ watero Yehova.”+