1 Akorinto 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ngati palibe womasulira, wa malilimeyo akhale chete mumpingo. Adzilankhule yekha mumtima+ ndipo alankhule kwa Mulungu.
28 Koma ngati palibe womasulira, wa malilimeyo akhale chete mumpingo. Adzilankhule yekha mumtima+ ndipo alankhule kwa Mulungu.