1 Akorinto 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mukupulumutsidwa+ ndi uthenga wabwino umenewo ngati mwaugwiritsitsa. Popanda kutero, ndiye kuti munakhala okhulupirira pachabe,+ malinga ndi mawu amene ndinakuuzani polengeza uthengawo kwa inu. 1 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:2 Nsanja ya Olonda,7/1/1998, ptsa. 14-15
2 Mukupulumutsidwa+ ndi uthenga wabwino umenewo ngati mwaugwiritsitsa. Popanda kutero, ndiye kuti munakhala okhulupirira pachabe,+ malinga ndi mawu amene ndinakuuzani polengeza uthengawo kwa inu.