2 Akorinto 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:12 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, tsa. 16
12 Sikuti tayambanso kudzichitira umboni+ tokha kwa inu ayi, koma tikukupatsani chifukwa chodzitamandira, ndipo chifukwacho ndifeyo,+ kuti muwayankhe amene amadzitama chifukwa cha maonekedwe akunja,+ osati chifukwa cha mtima.+