2 Akorinto 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tikusonyezanso zimenezi mwa kukhala oyera, odziwa zinthu, oleza mtima,+ okoma mtima,+ okhala ndi mzimu woyera, osonyeza chikondi chopanda chinyengo,+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:6 Nsanja ya Olonda,12/15/1998, ptsa. 19-20
6 Tikusonyezanso zimenezi mwa kukhala oyera, odziwa zinthu, oleza mtima,+ okoma mtima,+ okhala ndi mzimu woyera, osonyeza chikondi chopanda chinyengo,+