2 Akorinto 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni. 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:8 Nsanja ya Olonda,12/1/1989, ptsa. 24-26
8 Sindikukulamulani,+ koma ndikulankhula izi chifukwa cha khama limene ena asonyeza, kutinso ndione ngati chikondi chanu chilidi chenicheni.