2 Akorinto 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Munthu wokhala ndi zambiri sanakhale ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu wokhala ndi zochepa sanakhale ndi zocheperatu.”+ 2 Akorinto Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:15 Nsanja ya Olonda,1/15/1992, tsa. 17
15 Monga mmene Malemba amanenera kuti: “Munthu wokhala ndi zambiri sanakhale ndi zopitirira muyezo, ndipo munthu wokhala ndi zochepa sanakhale ndi zocheperatu.”+