2 Akorinto 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Si zokhazo, koma anaikidwanso+ ndi mipingo kuti akhale woyenda nafe pamene tikubweretsa mphatso zachifundozi. Tikupereka mphatsozi kuti zipereke ulemerero+ kwa Ambuye, komanso kuti tisonyeze kuti ndife ofunitsitsa kuthandiza ena.+
19 Si zokhazo, koma anaikidwanso+ ndi mipingo kuti akhale woyenda nafe pamene tikubweretsa mphatso zachifundozi. Tikupereka mphatsozi kuti zipereke ulemerero+ kwa Ambuye, komanso kuti tisonyeze kuti ndife ofunitsitsa kuthandiza ena.+