2 Akorinto 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano ponena za utumiki+ wothandiza oyerawo, n’zosafuna kuti ndichite kukulemberani.