Agalatiya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+
3 Kukoma mtima kwakukulu ndi mtendere zochokera kwa Mulungu Atate wathu, ndi Ambuye Yesu Khristu, zikhale nanu.+