Agalatiya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti ndikufuna mudziwe, abale, kuti uthenga wabwino umene ndinaulengeza monga uthenga wabwino sunachokere kwa anthu.+
11 Pakuti ndikufuna mudziwe, abale, kuti uthenga wabwino umene ndinaulengeza monga uthenga wabwino sunachokere kwa anthu.+