Agalatiya 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimene ndikukulemberanizi, ndikukuuzani pamaso pa Mulungu kuti sindikunama.+