Agalatiya 1:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene anali kutizunza kale uja,+ tsopano akulengeza uthenga wabwino wonena za chikhulupiriro chimene anali kuwononga.”+
23 Iwo ankangomva kuti: “Munthu amene anali kutizunza kale uja,+ tsopano akulengeza uthenga wabwino wonena za chikhulupiriro chimene anali kuwononga.”+