Agalatiya 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ifeyo ndife a mtundu wachiyuda.+ Si ife ochimwa+ ochokera mwa anthu a mitundu ina.