Agalatiya 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti ngakhale amene akudulidwawo sasunga Chilamulo,+ koma akufuna inuyo mudulidwe kuti iwo azidzitama chifukwa cha zimene zachitika pathupi lanu.
13 Pakuti ngakhale amene akudulidwawo sasunga Chilamulo,+ koma akufuna inuyo mudulidwe kuti iwo azidzitama chifukwa cha zimene zachitika pathupi lanu.