Aefeso 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mogwirizana ndi iyeyo tinaikidwa kukhala odzalandira cholowa,+ pakuti anatisankhiratu mwa kufuna kwake, iye amene amayendetsa zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,6/1/2006, ptsa. 23-24
11 Mogwirizana ndi iyeyo tinaikidwa kukhala odzalandira cholowa,+ pakuti anatisankhiratu mwa kufuna kwake, iye amene amayendetsa zinthu zonse mogwirizana ndi chifuniro chake.+