Aefeso 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:3 Nsanja ya Olonda,9/1/1995, tsa. 44/15/1987, ptsa. 10-11 Kukambitsirana, tsa. 360
3 Inde, tonsefe pa nthawi inayake pamene tinali pakati pawo, tinali kukhala motsatira zilakolako za thupi lathu.+ Tinali kuchita zofuna za thupi+ ndi maganizo, ndipo mwachibadwa tinali ana oyenera kulandira mkwiyo wa Mulungu,+ mofanana ndi ena onse.