Aefeso 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.
10 Pakuti ndife ntchito ya manja ake,+ ndipo tinalengedwa+ mogwirizana+ ndi Khristu Yesu kuti tichite ntchito zabwino,+ zimene Mulungu anakonzeratu+ kuti tiyendemo.