Aefeso 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+ Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:14 Nsanja ya Olonda,7/1/2008, tsa. 2111/15/1997, tsa. 285/15/1988, tsa. 1311/1/1987, tsa. 13
14 Pakuti iye ndiye mtendere wathu,+ amene analumikiza mbali ziwiri+ kukhala imodzi,+ ndi kugwetsa khoma+ lowalekanitsa limene linali pakati pawo.+