Aefeso 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chotero, simulinso anthu osadziwika+ kapena alendo m’dziko la eni,+ koma ndinu nzika+ zinzawo za oyerawo,+ ndipo ndinu a m’banja+ la Mulungu.
19 Chotero, simulinso anthu osadziwika+ kapena alendo m’dziko la eni,+ koma ndinu nzika+ zinzawo za oyerawo,+ ndipo ndinu a m’banja+ la Mulungu.