Aefeso 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndiponso kuti anandiululira chinsinsi chopatulika,+ monga ndalemba kale mwachidule.