Aefeso 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kudzera mwa iye, tili ndi ufulu wa kulankhula ndiponso njira yofikira Mulungu+ popanda kukayikira pokhala ndi chikhulupiriro mwa Yesuyo. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Nsanja ya Olonda,5/15/2006, tsa. 13
12 Kudzera mwa iye, tili ndi ufulu wa kulankhula ndiponso njira yofikira Mulungu+ popanda kukayikira pokhala ndi chikhulupiriro mwa Yesuyo.